Genesis 41:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Atatero, Farao anavula mphete yake yachifumu+ kudzanja lake, n’kuiveka kudzanja la Yosefe. Anamuvekanso malaya amtengo wapatali, ndi tcheni chagolide m’khosi mwake.+ Esitere 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 amubweretsere zovala zachifumu+ zimene mfumu imavala ndi hatchi* imene mfumu imakwera.+ Hatchiyo aiveke duku lachifumu. Luka 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Munthu winawake+ anali wolemera, ndipo nthawi zonse anali kuvala zovala zofiirira zapamwamba ndi nsalu zabwino kwambiri. Iye anali kusangalala ndi kudyerera tsiku ndi tsiku.+
42 Atatero, Farao anavula mphete yake yachifumu+ kudzanja lake, n’kuiveka kudzanja la Yosefe. Anamuvekanso malaya amtengo wapatali, ndi tcheni chagolide m’khosi mwake.+
8 amubweretsere zovala zachifumu+ zimene mfumu imavala ndi hatchi* imene mfumu imakwera.+ Hatchiyo aiveke duku lachifumu.
19 “Munthu winawake+ anali wolemera, ndipo nthawi zonse anali kuvala zovala zofiirira zapamwamba ndi nsalu zabwino kwambiri. Iye anali kusangalala ndi kudyerera tsiku ndi tsiku.+