-
Luka 16:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Panali munthu winawake wolemera amene ankakonda kuvala zovala zapepo ndi nsalu zabwino kwambiri. Iye ankasangalala komanso kudyerera tsiku ndi tsiku.
-