Oweruza 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atatero Mika anamuuza kuti: “Ukhale ndi ine ndipo uzitumikira ngati tate+ ndi wansembe+ wanga. Ine ndizikupatsa ndalama zasiliva 10 pa chaka, komanso zovala zako zoyenera ndi chakudya.” Pamenepo Mleviyo analowa m’nyumbamo. Yobu 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndinali bambo weniweni kwa osauka,+Ndipo mlandu wa munthu amene sindinali kumudziwa ndinkaufufuza.+ Salimo 105:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anamuika kukhala mkulu woyang’anira banja lake,+Komanso wolamulira chuma chake chonse.+
10 Atatero Mika anamuuza kuti: “Ukhale ndi ine ndipo uzitumikira ngati tate+ ndi wansembe+ wanga. Ine ndizikupatsa ndalama zasiliva 10 pa chaka, komanso zovala zako zoyenera ndi chakudya.” Pamenepo Mleviyo analowa m’nyumbamo.
16 Ndinali bambo weniweni kwa osauka,+Ndipo mlandu wa munthu amene sindinali kumudziwa ndinkaufufuza.+