Rute 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komano ngakhale kuti ndinedi wokuwombolani,+ pali wachibale wina wapafupi kwambiri kuposa ine+ amene angakuwombole.
12 Komano ngakhale kuti ndinedi wokuwombolani,+ pali wachibale wina wapafupi kwambiri kuposa ine+ amene angakuwombole.