Levitiko 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “‘M’bale wanu akasauka n’kugulitsa ena mwa malo ake, wowombola amene ndi wachibale wake wapafupi azibwera ndi kugulanso zimene m’bale wakeyo anagulitsa.+ Rute 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo Naomi anauza mpongozi wakeyo kuti: “Yehova amene sanaleke kusonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa amoyo ndi akufa,+ am’dalitse munthu ameneyu.”+ Ndipo Naomi anapitiriza kuti: “Munthuyutu ndi wachibale wathu.+ Ndi mmodzi wa otiwombola.”+
25 “‘M’bale wanu akasauka n’kugulitsa ena mwa malo ake, wowombola amene ndi wachibale wake wapafupi azibwera ndi kugulanso zimene m’bale wakeyo anagulitsa.+
20 Pamenepo Naomi anauza mpongozi wakeyo kuti: “Yehova amene sanaleke kusonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa amoyo ndi akufa,+ am’dalitse munthu ameneyu.”+ Ndipo Naomi anapitiriza kuti: “Munthuyutu ndi wachibale wathu.+ Ndi mmodzi wa otiwombola.”+