Rute 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Tsopano zinachitika kuti, m’masiku amene oweruza+ anali atsogoleri, m’dzikomo munagwa njala.+ Ndiyeno munthu wina anasamuka ku Betelehemu+ wa ku Yuda kukakhala m’dziko la Mowabu+ monga mlendo. Anasamuka ndi mkazi wake ndi ana ake awiri aamuna. Rute 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo iye limodzi ndi apongozi ake anakonzekera ulendo wochoka kudziko la Mowabu, chifukwa ali kumeneko anamva kuti Yehova wakumbukira anthu ake+ powapatsa chakudya.+
1 Tsopano zinachitika kuti, m’masiku amene oweruza+ anali atsogoleri, m’dzikomo munagwa njala.+ Ndiyeno munthu wina anasamuka ku Betelehemu+ wa ku Yuda kukakhala m’dziko la Mowabu+ monga mlendo. Anasamuka ndi mkazi wake ndi ana ake awiri aamuna.
6 Pamenepo iye limodzi ndi apongozi ake anakonzekera ulendo wochoka kudziko la Mowabu, chifukwa ali kumeneko anamva kuti Yehova wakumbukira anthu ake+ powapatsa chakudya.+