Deuteronomo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zikatero mkazi wamasiyeyo aziyandikira m’bale wa mwamuna wakeyo akuluwo akuona ndipo azim’vula nsapato+ ndi kumulavulira kumaso.+ Pamenepo azinena kuti, ‘Izi ndiye zoyenera kuchitikira munthu wokana kumanga nyumba ya m’bale wake.’+
9 Zikatero mkazi wamasiyeyo aziyandikira m’bale wa mwamuna wakeyo akuluwo akuona ndipo azim’vula nsapato+ ndi kumulavulira kumaso.+ Pamenepo azinena kuti, ‘Izi ndiye zoyenera kuchitikira munthu wokana kumanga nyumba ya m’bale wake.’+