Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 28:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mulungu Wamphamvuyonse adzakudalitsa. Adzakupatsa ana ndipo adzawachulukitsa moti adzakhala mitundu yambiri ya anthu.+

  • Genesis 35:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ana aamuna amene Leya anaberekera Yakobo anali Rubeni+ mwana wake woyamba, Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara ndi Zebuloni.

  • Genesis 35:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ana amene Rakele anaberekera Yakobo anali Yosefe ndi Benjamini.

  • Genesis 46:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Amenewa ndiwo anali ana a Leya,+ amene anaberekera Yakobo ku Padana-ramu, kuphatikizapo Dina+ mwana wamkazi wa Yakobo. Ana ake onse aamuna ndi aakazi ndi adzukulu ake analipo 33.

  • Genesis 46:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Amenewa ndiwo anali ana a Zilipa,+ yemwe Labani anam’pereka kwa mwana wake wamkazi Leya. Ndiwo ana amene Zilipa anaberekera Yakobo m’kupita kwa nthawi. Onse pamodzi analipo 16.

  • Genesis 46:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Amenewa ndiwo ana amene Rakele anaberekera Yakobo. Onse pamodzi analipo 14.

  • Genesis 46:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Amenewa ndiwo anali ana a Biliha,+ yemwe Labani anam’pereka kwa mwana wake wamkazi Rakele. Awa ndiwo ana amene Biliha anaberekera Yakobo m’kupita kwa nthawi. Onse pamodzi analipo 7.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena