1 Samueli 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Davide anathawa+ kuchoka ku Nayoti, ku Rama. Koma anapita kwa Yonatani ndi kumuuza kuti: “Kodi ine ndachita chiyani?+ Ndalakwanji, ndipo bambo ako ndawachimwira chiyani kuti azindifunafuna kuti andiphe?”
20 Ndiyeno Davide anathawa+ kuchoka ku Nayoti, ku Rama. Koma anapita kwa Yonatani ndi kumuuza kuti: “Kodi ine ndachita chiyani?+ Ndalakwanji, ndipo bambo ako ndawachimwira chiyani kuti azindifunafuna kuti andiphe?”