Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Zitatero, Sauli anafuna kulasa Davide kuti amukhomerere kukhoma ndi mkondo.+ Koma Davide anaulewa+ pamaso pa Sauli, moti mkondowo unalasa khoma. Pamenepo, Davide anathawa kuti adzipulumutse usiku umenewo.+

  • 1 Samueli 23:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kenako Sauli anakhala mbali imodzi ya phiri ndipo Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anali mbali inanso ya phirilo. Zitatero Davide ananyamuka mofulumira kuti athawe+ Sauli. Pa nthawiyi n’kuti Sauli ndi asilikali ake atatsala pang’ono kupeza ndi kugwira Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye.+

  • 2 Petulo 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena