1 Samueli 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Davide anathawa ndi kupulumuka,+ moti anafika kwa Samueli ku Rama.+ Atafika kumeneko anasimbira Samueli zonse zimene Sauli anam’chitira. Kenako Davide ndi Samueli anachoka ndi kupita kukakhala ku Nayoti.+
18 Choncho Davide anathawa ndi kupulumuka,+ moti anafika kwa Samueli ku Rama.+ Atafika kumeneko anasimbira Samueli zonse zimene Sauli anam’chitira. Kenako Davide ndi Samueli anachoka ndi kupita kukakhala ku Nayoti.+