2 Samueli 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mtima wanga ukuwawa chifukwa cha iwe m’bale wanga Yonatani,Unali wosangalatsa kwambiri kwa ine.+Chikondi chako chinali chapamwamba kwambiri kuposa chikondi cha akazi.+
26 Mtima wanga ukuwawa chifukwa cha iwe m’bale wanga Yonatani,Unali wosangalatsa kwambiri kwa ine.+Chikondi chako chinali chapamwamba kwambiri kuposa chikondi cha akazi.+