1 Samueli 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Doegi,+ Mwedomu, amene anali mkulu wa atumiki a Sauli anayankha kuti: “Ineyo ndinaona mwana wa Jese atabwera ku Nobu kwa Ahimeleki,+ mwana wa Ahitubu.+
9 Pamenepo Doegi,+ Mwedomu, amene anali mkulu wa atumiki a Sauli anayankha kuti: “Ineyo ndinaona mwana wa Jese atabwera ku Nobu kwa Ahimeleki,+ mwana wa Ahitubu.+