Genesis 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anadalitsa Abulamu kuti: “Mulungu Wam’mwambamwamba adalitse Abulamu,+Iye amene anapanga kumwamba ndi dziko lapansi.+ Numeri 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Lankhula ndi Aroni ndiponso ana ake kuti, ‘Muzidalitsa+ ana a Isiraeli motere:
19 Kenako anadalitsa Abulamu kuti: “Mulungu Wam’mwambamwamba adalitse Abulamu,+Iye amene anapanga kumwamba ndi dziko lapansi.+ Numeri 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Lankhula ndi Aroni ndiponso ana ake kuti, ‘Muzidalitsa+ ana a Isiraeli motere: