1 Samueli 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndipo ine ndikum’pereka* kwa Yehova.+ Ndam’pereka kwa Yehova masiku onse a moyo wake.” Pamenepo iye* anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi pamaso pa Yehova.+
28 Ndipo ine ndikum’pereka* kwa Yehova.+ Ndam’pereka kwa Yehova masiku onse a moyo wake.” Pamenepo iye* anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi pamaso pa Yehova.+