Oweruza 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 ine ndidzapereka kwa Yehova+ aliyense amene adzatuluka m’nyumba yanga kudzandichingamira pamene ndikubwera mwamtendere+ kuchokera kwa ana a Amoni. Ndidzam’pereka monga nsembe yopsereza.”+
31 ine ndidzapereka kwa Yehova+ aliyense amene adzatuluka m’nyumba yanga kudzandichingamira pamene ndikubwera mwamtendere+ kuchokera kwa ana a Amoni. Ndidzam’pereka monga nsembe yopsereza.”+