1 Mbiri 2:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ana a Kalebe+ m’bale wake wa Yerameeli anali Mesa mwana wake woyamba, yemwe anali bambo wa Zifi, ndi ana a Maresha bambo wa Heburoni.
42 Ana a Kalebe+ m’bale wake wa Yerameeli anali Mesa mwana wake woyamba, yemwe anali bambo wa Zifi, ndi ana a Maresha bambo wa Heburoni.