1 Samueli 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma Sauli anapita kwawo ku Gibeya,+ ndipo amuna olimba mtima amene Mulungu anakhudza mitima yawo anapita naye pamodzi.+ 1 Samueli 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Tsopano Samueli ananyamuka kupita ku Rama, koma Sauli anapita kunyumba kwake ku Gibeya.+
26 Koma Sauli anapita kwawo ku Gibeya,+ ndipo amuna olimba mtima amene Mulungu anakhudza mitima yawo anapita naye pamodzi.+