Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 18:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea,+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake.

      Ichi chinali cholowa cha ana a Benjamini potsata mabanja awo.+

  • Oweruza 20:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndiyeno ana a Benjamini anasonkhana pamodzi ku Gibeya, kuchokera m’mizinda, kuti akamenyane ndi ana a Isiraeli.

  • 1 Samueli 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mithengayo inafika ku Gibeya,+ kwawo kwa Sauli, ndi kuuza anthu uthengawo. Anthu onse atamva uthengawo anayamba kulira mokweza mawu.+

  • 1 Samueli 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Sauli anadzisankhira amuna 3,000 a mu Isiraeli. Amuna 2,000 anali ndi Sauliyo ku Mikimasi+ ndi kudera lamapiri la Beteli. Amuna 1,000 anali ndi Yonatani+ ku Gibeya+ wa ku Benjamini, ndipo anthu ena onse otsalawo anawabweza kumahema awo.

  • 2 Samueli 21:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 mutipatse ana ake aamuna 7,+ ndipo tionetse+ mitembo yawo kwa Yehova mwa kuipachika ku Gibeya,+ kwawo kwa Sauli, munthu amene Yehova+ anamusankha kukhala mfumu.” Pamenepo mfumu inati: “Ndiwapereka m’manja mwanu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena