Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 15:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kuchokera pamenepo, anapitirira mpaka kuchigwa cha mwana wa Hinomu,+ kumalo otsetsereka otchedwa Yebusi+ kum’mwera, kutanthauza Yerusalemu.+ Anapitirirabe mpaka pamwamba pa phiri loyang’anizana ndi chigwa cha Hinomu, limene lili kumadzulo kwa chigwacho. Phirilo lili kumpoto kwa chigwa cha Arefai,+ kumapeto kwa chigwacho.

  • Oweruza 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma mwamunayo sanavomere kuti agone, ndipo ananyamuka ndi kuyamba ulendo wake. Iye anayenda mpaka kukafika pafupi ndi Yebusi,+ amene ndi Yerusalemu.+ Pa ulendowu, anali ndi abulu awiri amphongo aja, okhala ndi zishalo, ndipo analinso ndi mdzakazi wake ndi mtumiki wake.

  • 1 Mbiri 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pambuyo pake Davide ndi Aisiraeli onse anapita ku Yerusalemu,+ kapena kuti ku Yebusi,+ dziko limene kunali kukhala Ayebusi.+

  • 2 Mbiri 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako Solomo anayamba kumanga nyumba ya Yehova+ ku Yerusalemu paphiri la Moriya,+ pamalo amene Yehova anaonekera kwa Davide bambo ake.+ Anamanga nyumbayo pamalo amene Davide anali atakonza. Amenewa anali malo opunthira mbewu a Orinani+ Myebusi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena