Yoswa 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea,+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake. Ichi chinali cholowa cha ana a Benjamini potsata mabanja awo.+ Oweruza 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana a Benjamini sanapitikitse Ayebusi amene anali kukhala m’Yerusalemu,+ moti Ayebusiwo akukhalabe ndi ana a Benjamini m’Yerusalemu kufikira lero.+
28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea,+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake. Ichi chinali cholowa cha ana a Benjamini potsata mabanja awo.+
21 Ana a Benjamini sanapitikitse Ayebusi amene anali kukhala m’Yerusalemu,+ moti Ayebusiwo akukhalabe ndi ana a Benjamini m’Yerusalemu kufikira lero.+