Oweruza 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Poyankha mbuye wakeyo anati: “Tisapatukire mumzinda wa anthu achilendo+ amene si ana a Isiraeli. Tiyeni tipitirire ndi kukafika ku Gibeya.”+ 1 Samueli 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma Sauli anapita kwawo ku Gibeya,+ ndipo amuna olimba mtima amene Mulungu anakhudza mitima yawo anapita naye pamodzi.+
12 Poyankha mbuye wakeyo anati: “Tisapatukire mumzinda wa anthu achilendo+ amene si ana a Isiraeli. Tiyeni tipitirire ndi kukafika ku Gibeya.”+
26 Koma Sauli anapita kwawo ku Gibeya,+ ndipo amuna olimba mtima amene Mulungu anakhudza mitima yawo anapita naye pamodzi.+