Yoswa 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea,+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake. Ichi chinali cholowa cha ana a Benjamini potsata mabanja awo.+ 1 Samueli 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma Sauli anapita kwawo ku Gibeya,+ ndipo amuna olimba mtima amene Mulungu anakhudza mitima yawo anapita naye pamodzi.+ Yesaya 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Wadutsa powolokera mtsinje. Usiku agona ku Geba.+ Rama+ wanjenjemera ndipo Gibeya,+ kwawo kwa Sauli, wathawa. Hoseya 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Lizani lipenga la nyanga ya nkhosa+ ku Gibeya!+ Lizani lipenga ku Rama! Fuulani mfuu ya nkhondo ku Beti-aveni!+ Tili pambuyo pako, iwe Benjamini!+
28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea,+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake. Ichi chinali cholowa cha ana a Benjamini potsata mabanja awo.+
26 Koma Sauli anapita kwawo ku Gibeya,+ ndipo amuna olimba mtima amene Mulungu anakhudza mitima yawo anapita naye pamodzi.+
29 Wadutsa powolokera mtsinje. Usiku agona ku Geba.+ Rama+ wanjenjemera ndipo Gibeya,+ kwawo kwa Sauli, wathawa.
8 “Lizani lipenga la nyanga ya nkhosa+ ku Gibeya!+ Lizani lipenga ku Rama! Fuulani mfuu ya nkhondo ku Beti-aveni!+ Tili pambuyo pako, iwe Benjamini!+