Hoseya 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Lizani lipenga la nyanga ya nkhosa+ ku Gibeya!+ Lizani lipenga ku Rama! Fuulani mfuu ya nkhondo ku Beti-aveni!+ Tili pambuyo pako, iwe Benjamini!+
8 “Lizani lipenga la nyanga ya nkhosa+ ku Gibeya!+ Lizani lipenga ku Rama! Fuulani mfuu ya nkhondo ku Beti-aveni!+ Tili pambuyo pako, iwe Benjamini!+