Yoswa 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kefara-amoni, Ofini, ndi Geba.+ Mizinda 12 ndi midzi yake. Yoswa 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuchokera m’fuko la Benjamini, anawapatsa Gibeoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Geba+ ndi malo ake odyetserako ziweto, 2 Mbiri 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno mfumu Asa inatenga Ayuda onse,+ ndipo iwo anapita kukatenga miyala ya ku Rama+ ndi matabwa ake, zimene Basa ankamangira.+ Mfumuyo inatenga zinthu zimenezo n’kuyamba kukamangira Geba+ ndi Mizipa.+
17 Kuchokera m’fuko la Benjamini, anawapatsa Gibeoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Geba+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
6 Ndiyeno mfumu Asa inatenga Ayuda onse,+ ndipo iwo anapita kukatenga miyala ya ku Rama+ ndi matabwa ake, zimene Basa ankamangira.+ Mfumuyo inatenga zinthu zimenezo n’kuyamba kukamangira Geba+ ndi Mizipa.+