2 Samueli 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako anaika mafupa a Sauli ndi Yonatani mwana wake m’dziko la Benjamini ku Zela+ m’manda a Kisi+ bambo ake, kuti achite zonse zimene mfumu inalamula. Izi zitachitika, Mulungu anamvetsera kuchonderera kwawo kuti amvere chisoni dziko lawo.+
14 Kenako anaika mafupa a Sauli ndi Yonatani mwana wake m’dziko la Benjamini ku Zela+ m’manda a Kisi+ bambo ake, kuti achite zonse zimene mfumu inalamula. Izi zitachitika, Mulungu anamvetsera kuchonderera kwawo kuti amvere chisoni dziko lawo.+