1 Samueli 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano panali mwamuna wina wochokera kudera la Benjamini dzina lake Kisi,+ mwana wa Abiyeli, mwana wa Zerori, mwana wa Bekorati, mwana wa Afiya. Iye anali wa fuko la Benjamini+ ndipo anali mwamuna wachuma kwambiri.+ 1 Samueli 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno onse amene anali kumudziwa atamuona, anadabwa kuona kuti ali pakati pa aneneri ndipo akulankhula ngati mneneri. Choncho anthuwo anayamba kufunsana kuti: “Kodi chachitikira mwana wa Kisi n’chiyani? Kodi Sauli nayenso ndi mmodzi wa aneneri?”+
9 Tsopano panali mwamuna wina wochokera kudera la Benjamini dzina lake Kisi,+ mwana wa Abiyeli, mwana wa Zerori, mwana wa Bekorati, mwana wa Afiya. Iye anali wa fuko la Benjamini+ ndipo anali mwamuna wachuma kwambiri.+
11 Ndiyeno onse amene anali kumudziwa atamuona, anadabwa kuona kuti ali pakati pa aneneri ndipo akulankhula ngati mneneri. Choncho anthuwo anayamba kufunsana kuti: “Kodi chachitikira mwana wa Kisi n’chiyani? Kodi Sauli nayenso ndi mmodzi wa aneneri?”+