1 Samueli 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Sauli nayenso anavula zovala zake, ndipo nayenso anayamba kuchita zinthu ngati mneneri pamaso pa Samueli. Iye anagwa pansi ndi kugona pomwepo ali wosavala* usana wonse ndi usiku wonse.+ N’chifukwa chake pali mawu okuluwika akuti: “Kodi Sauli nayenso ndi mmodzi wa aneneri?”+ Mateyu 13:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Atafika m’dera lakwawo+ anayamba kuwaphunzitsa m’sunagoge wawo,+ moti anthu anadabwa ndipo anali kunena kuti: “Kodi munthu ameneyu, nzeru ndi ntchito zamphamvu zoterezi anazitenga kuti? Machitidwe 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo pamene onse amene anakhala m’bwalo la Khoti Lalikulu la Ayuda anamuyang’anitsitsa,+ anaona kuti nkhope yake inali ngati nkhope ya mngelo.+
24 Sauli nayenso anavula zovala zake, ndipo nayenso anayamba kuchita zinthu ngati mneneri pamaso pa Samueli. Iye anagwa pansi ndi kugona pomwepo ali wosavala* usana wonse ndi usiku wonse.+ N’chifukwa chake pali mawu okuluwika akuti: “Kodi Sauli nayenso ndi mmodzi wa aneneri?”+
54 Atafika m’dera lakwawo+ anayamba kuwaphunzitsa m’sunagoge wawo,+ moti anthu anadabwa ndipo anali kunena kuti: “Kodi munthu ameneyu, nzeru ndi ntchito zamphamvu zoterezi anazitenga kuti?
15 Ndipo pamene onse amene anakhala m’bwalo la Khoti Lalikulu la Ayuda anamuyang’anitsitsa,+ anaona kuti nkhope yake inali ngati nkhope ya mngelo.+