Yoswa 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pambuyo pake, anaunjika mulu waukulu wa miyala pa iye. Muluwo ulipo mpaka lero.+ Zitatero, mkwiyo waukulu wa Yehova unatha.+ Ndiye chifukwa chake malowo anatchedwa chigwa cha Akori*+ mpaka lero. 2 Samueli 24:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero, Davide anamangira Yehova guwa lansembe+ pamenepo ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano. Choncho Yehova anamva kuchonderera kwawo,+ moti mliriwo anauthetsa mu Isiraeli.
26 Pambuyo pake, anaunjika mulu waukulu wa miyala pa iye. Muluwo ulipo mpaka lero.+ Zitatero, mkwiyo waukulu wa Yehova unatha.+ Ndiye chifukwa chake malowo anatchedwa chigwa cha Akori*+ mpaka lero.
25 Zitatero, Davide anamangira Yehova guwa lansembe+ pamenepo ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano. Choncho Yehova anamva kuchonderera kwawo,+ moti mliriwo anauthetsa mu Isiraeli.