Yoswa 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea,+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake. Ichi chinali cholowa cha ana a Benjamini potsata mabanja awo.+ Oweruza 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno ana a Yuda anapitiriza kumenyana ndi mzinda wa Yerusalemu+ n’kuulanda. Anapha anthu okhala mmenemo ndi lupanga, ndipo mzindawo anautentha ndi moto.
28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea,+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake. Ichi chinali cholowa cha ana a Benjamini potsata mabanja awo.+
8 Ndiyeno ana a Yuda anapitiriza kumenyana ndi mzinda wa Yerusalemu+ n’kuulanda. Anapha anthu okhala mmenemo ndi lupanga, ndipo mzindawo anautentha ndi moto.