2 Samueli 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Gadi anafika kwa Davide tsiku limenelo ndi kumuuza kuti: “Pita ukamangire Yehova guwa lansembe pamalo opunthira mbewu a Arauna Myebusi.”+ 1 Mbiri 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Davide anauza Orinani kuti: “Ndipatse malo ako opunthira mbewuwa kuti ndimangirepo Yehova guwa lansembe, kuti mliriwu+ uthe pakati pa anthuwa. Ndikupatsa ndalama+ zake zonse.”+
18 Kenako Gadi anafika kwa Davide tsiku limenelo ndi kumuuza kuti: “Pita ukamangire Yehova guwa lansembe pamalo opunthira mbewu a Arauna Myebusi.”+
22 Kenako Davide anauza Orinani kuti: “Ndipatse malo ako opunthira mbewuwa kuti ndimangirepo Yehova guwa lansembe, kuti mliriwu+ uthe pakati pa anthuwa. Ndikupatsa ndalama+ zake zonse.”+