1 Mbiri 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno mngelo wa Yehova anauza Gadi+ kuti auze Davide kuti Davideyo apite kumalo opunthira mbewu a Orinani Myebusi, n’kukamanga guwa lansembe la Yehova.+ 2 Mbiri 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Solomo anayamba kumanga nyumba ya Yehova+ ku Yerusalemu paphiri la Moriya,+ pamalo amene Yehova anaonekera kwa Davide bambo ake.+ Anamanga nyumbayo pamalo amene Davide anali atakonza. Amenewa anali malo opunthira mbewu a Orinani+ Myebusi.
18 Ndiyeno mngelo wa Yehova anauza Gadi+ kuti auze Davide kuti Davideyo apite kumalo opunthira mbewu a Orinani Myebusi, n’kukamanga guwa lansembe la Yehova.+
3 Kenako Solomo anayamba kumanga nyumba ya Yehova+ ku Yerusalemu paphiri la Moriya,+ pamalo amene Yehova anaonekera kwa Davide bambo ake.+ Anamanga nyumbayo pamalo amene Davide anali atakonza. Amenewa anali malo opunthira mbewu a Orinani+ Myebusi.