2 Samueli 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Gadi anafika kwa Davide tsiku limenelo ndi kumuuza kuti: “Pita ukamangire Yehova guwa lansembe pamalo opunthira mbewu a Arauna Myebusi.”+ 2 Mbiri 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Solomo anayamba kumanga nyumba ya Yehova+ ku Yerusalemu paphiri la Moriya,+ pamalo amene Yehova anaonekera kwa Davide bambo ake.+ Anamanga nyumbayo pamalo amene Davide anali atakonza. Amenewa anali malo opunthira mbewu a Orinani+ Myebusi.
18 Kenako Gadi anafika kwa Davide tsiku limenelo ndi kumuuza kuti: “Pita ukamangire Yehova guwa lansembe pamalo opunthira mbewu a Arauna Myebusi.”+
3 Kenako Solomo anayamba kumanga nyumba ya Yehova+ ku Yerusalemu paphiri la Moriya,+ pamalo amene Yehova anaonekera kwa Davide bambo ake.+ Anamanga nyumbayo pamalo amene Davide anali atakonza. Amenewa anali malo opunthira mbewu a Orinani+ Myebusi.