Genesis 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mulungu anapitiriza kuti: “Tenga Isaki+ mwana wako mmodzi yekhayo, mwana wako amene umamukonda kwambiriyo,+ ndipo muyende ulendo wopita ku Moriya.+ Kumeneko ukamupereke nsembe yopsereza paphiri limene ndidzakuuza.”+ Genesis 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero Abulahamu anatcha malowo Yehova-yire.* Ndiye chifukwa chake lero pali mawu akuti: “M’phiri lake Yehova adzapereka zinthu zofunikira.”+
2 Mulungu anapitiriza kuti: “Tenga Isaki+ mwana wako mmodzi yekhayo, mwana wako amene umamukonda kwambiriyo,+ ndipo muyende ulendo wopita ku Moriya.+ Kumeneko ukamupereke nsembe yopsereza paphiri limene ndidzakuuza.”+
14 Chotero Abulahamu anatcha malowo Yehova-yire.* Ndiye chifukwa chake lero pali mawu akuti: “M’phiri lake Yehova adzapereka zinthu zofunikira.”+