Miyambo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ine ndinali mwana wabwino kwa bambo anga.+ Ndinali wokondedwa kwambiri ndiponso mmodzi yekhayo pamaso pa mayi anga.+ Miyambo 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ine ndinali pambali pake monga mmisiri waluso.+ Tsiku ndi tsiku, iye anali kusangalala kwambiri ndi ine.+ Ineyo ndinkakhala wosangalala pamaso pake nthawi zonse.+ Yohane 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Pakuti Mulungu anakonda+ kwambiri dziko mwakuti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense wokhulupirira+ iye asawonongeke,+ koma akhale ndi moyo wosatha.+ Yohane 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chimene Atate amandikondera n’chakuti,+ ndikupereka moyo wanga+ kuti ndikaulandirenso.
3 Pakuti ine ndinali mwana wabwino kwa bambo anga.+ Ndinali wokondedwa kwambiri ndiponso mmodzi yekhayo pamaso pa mayi anga.+
30 ine ndinali pambali pake monga mmisiri waluso.+ Tsiku ndi tsiku, iye anali kusangalala kwambiri ndi ine.+ Ineyo ndinkakhala wosangalala pamaso pake nthawi zonse.+
16 “Pakuti Mulungu anakonda+ kwambiri dziko mwakuti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense wokhulupirira+ iye asawonongeke,+ koma akhale ndi moyo wosatha.+