-
Yoswa 15:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kuchokera pamenepo, anapitirira mpaka kuchigwa cha mwana wa Hinomu,+ kumalo otsetsereka otchedwa Yebusi+ kumʼmwera, kutanthauza Yerusalemu.+ Anapitirirabe mpaka pamwamba pa phiri loyangʼanizana ndi chigwa cha Hinomu, limene lili kumadzulo kwa chigwacho. Phirilo lili kumpoto kwa chigwa cha Arefai, kumapeto kwa chigwacho.
-