Oweruza 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mngelo wa Yehova atalankhula mawu amenewa kwa ana onse a Isiraeli, anthuwo anayamba kulira mokweza mawu.+ Oweruza 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anthuwo anapita ku Beteli+ ndi kukhala pansi kumeneko pamaso pa Mulungu woona+ mpaka madzulo. Iwo anali kulira kwambiri mofuula.+ 1 Samueli 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Davide ndi anthu amene anali naye anayamba kulira mofuula+ mpaka kulefuka osathanso kulira.
4 Mngelo wa Yehova atalankhula mawu amenewa kwa ana onse a Isiraeli, anthuwo anayamba kulira mokweza mawu.+
2 Ndiyeno anthuwo anapita ku Beteli+ ndi kukhala pansi kumeneko pamaso pa Mulungu woona+ mpaka madzulo. Iwo anali kulira kwambiri mofuula.+
4 Pamenepo Davide ndi anthu amene anali naye anayamba kulira mofuula+ mpaka kulefuka osathanso kulira.