1 Samueli 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo Sauli anasiya kum’thamangitsa Davide+ ndipo anabwerera kukakumana ndi Afilisiti. N’chifukwa chake malowo anawatcha Thanthwe Logawanitsa.
28 Pamenepo Sauli anasiya kum’thamangitsa Davide+ ndipo anabwerera kukakumana ndi Afilisiti. N’chifukwa chake malowo anawatcha Thanthwe Logawanitsa.