Salimo 57:kam Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Kwa wotsogolera nyimbo. “Musandiwononge.” Salimo la Davide. Mikitamu.* Pa nthawi imene anathawa Sauli n’kukalowa m’phanga.+ Salimo 142:kam Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Masikili.* Salimo ndiponso pemphero la Davide, pamene anali kukhala kuphanga.+
Kwa wotsogolera nyimbo. “Musandiwononge.” Salimo la Davide. Mikitamu.* Pa nthawi imene anathawa Sauli n’kukalowa m’phanga.+