1 Samueli 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Sauli anazindikira mawu a Davide, ndipo anati: “Kodi ndi mawu ako, mwana wanga Davide?”+ Davide anayankha kuti: “Inde ndi mawu anga, mbuyanga mfumu.”
17 Pamenepo Sauli anazindikira mawu a Davide, ndipo anati: “Kodi ndi mawu ako, mwana wanga Davide?”+ Davide anayankha kuti: “Inde ndi mawu anga, mbuyanga mfumu.”