1 Samueli 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake, Davide nayenso anatuluka m’phangamo ndi kuitana Sauli kuti: “Mbuyanga+ mfumu!” Pamenepo Sauli anacheuka ndipo Davide anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+ 1 Samueli 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno Davide atangomaliza kulankhula mawu amenewa kwa Sauli, Sauli anati: “Kodi ndi mawu ako, mwana wanga Davide?”+ Pamenepo Sauli anayamba kulira mokweza mawu.+
8 Pambuyo pake, Davide nayenso anatuluka m’phangamo ndi kuitana Sauli kuti: “Mbuyanga+ mfumu!” Pamenepo Sauli anacheuka ndipo Davide anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+
16 Ndiyeno Davide atangomaliza kulankhula mawu amenewa kwa Sauli, Sauli anati: “Kodi ndi mawu ako, mwana wanga Davide?”+ Pamenepo Sauli anayamba kulira mokweza mawu.+