Genesis 27:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pamenepo Esau anafunsa bambo ake kuti: “Bambo, ngakhale limodzi dalitso silinatsaleko? Bambo ndidalitseni, ndidalitseni inenso chonde!”+ Esau atatero analira mofuula kwambiri, misozi ili mbwembwembwe.+
38 Pamenepo Esau anafunsa bambo ake kuti: “Bambo, ngakhale limodzi dalitso silinatsaleko? Bambo ndidalitseni, ndidalitseni inenso chonde!”+ Esau atatero analira mofuula kwambiri, misozi ili mbwembwembwe.+