Aheberi 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mukudziwa kuti pambuyo pake, atafunanso kulandira dalitso monga cholowa chake,+ anamukanira.+ Pakuti ngakhale kuti anayesetsa ndi mtima wonse, kwinaku akugwetsa misozi,+ kuti bambo ake asinthe maganizo, sizinatheke.+
17 Mukudziwa kuti pambuyo pake, atafunanso kulandira dalitso monga cholowa chake,+ anamukanira.+ Pakuti ngakhale kuti anayesetsa ndi mtima wonse, kwinaku akugwetsa misozi,+ kuti bambo ake asinthe maganizo, sizinatheke.+