Genesis 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo iye anamuyankha Loti kuti: “Chabwino, ndavomera zimene wapempha.+ Sindiwononga mzinda umene wanenawo.+ Miyambo 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Wodzudzula munthu,+ patsogolo pake adzakondedwa kwambiri kuposa amene amakokomeza ndi lilime lake ponena zinthu zabwino za wina.
21 Pamenepo iye anamuyankha Loti kuti: “Chabwino, ndavomera zimene wapempha.+ Sindiwononga mzinda umene wanenawo.+
23 Wodzudzula munthu,+ patsogolo pake adzakondedwa kwambiri kuposa amene amakokomeza ndi lilime lake ponena zinthu zabwino za wina.