Genesis 24:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Atatha kum’dalitsa, Rabeka ndi adzakazi ake+ ananyamuka n’kukwera ngamila+ kumapita limodzi ndi mtumiki wa Abulahamu uja. Motero mtumikiyo anatenga Rabeka n’kupita naye.
61 Atatha kum’dalitsa, Rabeka ndi adzakazi ake+ ananyamuka n’kukwera ngamila+ kumapita limodzi ndi mtumiki wa Abulahamu uja. Motero mtumikiyo anatenga Rabeka n’kupita naye.