1 Samueli 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso chaka ndi chaka mayi ake anali kumusokera kamalaya kakunja kodula manja. Iwo anali kumubweretsera kamalayako akabwera ndi mwamuna wawo kudzapereka nsembe ya pachaka.+
19 Komanso chaka ndi chaka mayi ake anali kumusokera kamalaya kakunja kodula manja. Iwo anali kumubweretsera kamalayako akabwera ndi mwamuna wawo kudzapereka nsembe ya pachaka.+