Yoswa 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Gawo+ la fuko la ana a Yuda potsata mabanja awo linkafika kumalire a Edomu,+ ndi kuchipululu cha Zini,+ mpaka kothera kwa Negebu,+ kum’mwera. Yobu 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuti mfuu yachisangalalo ya anthu oipa sikhalitsa,+Ndiponso kuti kusangalala kwa wampatuko kumakhala kwa kanthawi?
15 Gawo+ la fuko la ana a Yuda potsata mabanja awo linkafika kumalire a Edomu,+ ndi kuchipululu cha Zini,+ mpaka kothera kwa Negebu,+ kum’mwera.
5 Kuti mfuu yachisangalalo ya anthu oipa sikhalitsa,+Ndiponso kuti kusangalala kwa wampatuko kumakhala kwa kanthawi?