1 Samueli 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Davide pamodzi ndi amuna 400 anapitiriza kuwathamangitsa,+ koma amuna 200 amene anatopa kwambiri ndipo sanathe kuwoloka chigwa cha Besori+ anaima pomwepo.
10 Davide pamodzi ndi amuna 400 anapitiriza kuwathamangitsa,+ koma amuna 200 amene anatopa kwambiri ndipo sanathe kuwoloka chigwa cha Besori+ anaima pomwepo.