Yoswa 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ndiponso midzi yonse yozungulira mizinda imeneyi mpaka kukafika ku Baalati-beere,+ komwe ndi ku Rama+ wa kum’mwera. Ichi chinali cholowa cha fuko la ana a Simiyoni potsata mabanja awo.
8 ndiponso midzi yonse yozungulira mizinda imeneyi mpaka kukafika ku Baalati-beere,+ komwe ndi ku Rama+ wa kum’mwera. Ichi chinali cholowa cha fuko la ana a Simiyoni potsata mabanja awo.