Genesis 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+ Genesis 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Aamori, Akanani, Agirigasi ndi la Ayebusi.”+ Oweruza 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “‘Choncho ndi Yehova Mulungu wa Aisiraeli amene anagonjetsa Aamori pamaso pa anthu ake Aisiraeli,+ ndipo iwe ukufuna kuwagonjetsa.
18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+
23 “‘Choncho ndi Yehova Mulungu wa Aisiraeli amene anagonjetsa Aamori pamaso pa anthu ake Aisiraeli,+ ndipo iwe ukufuna kuwagonjetsa.